Salimo 49:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mtundu wa anthu ndiponso inu ana a anthu,Inu olemera pamodzi ndi inu osauka.+ Miyambo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu wosauka ndiponso munthu wozunza ena n’chimodzimodzi,+ koma Yehova amawalitsa maso a onsewa.+
13 Munthu wosauka ndiponso munthu wozunza ena n’chimodzimodzi,+ koma Yehova amawalitsa maso a onsewa.+