Miyambo 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene walonjeza kuti adzapereka ngongole ya mlendo iye akadzalephera kubweza,+ zinthu sizidzamuyendera bwino. Koma wodana ndi kugwirana chanza pochita mgwirizano sakhala ndi nkhawa. Miyambo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+
15 Munthu amene walonjeza kuti adzapereka ngongole ya mlendo iye akadzalephera kubweza,+ zinthu sizidzamuyendera bwino. Koma wodana ndi kugwirana chanza pochita mgwirizano sakhala ndi nkhawa.
18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+