Deuteronomo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usasunthe zizindikiro za malire a mnzako,+ makolo anu ataika kale malire a cholowa chimene udzalandira, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako.
14 “Usasunthe zizindikiro za malire a mnzako,+ makolo anu ataika kale malire a cholowa chimene udzalandira, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako.