Salimo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Masoka a munthu wolungama ndi ochuluka,+Koma Yehova amamupulumutsa ku masoka onsewo.+ 2 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anatipulumutsadi ku chinthu choopsa, ndicho imfa, ndipo adzatipulumutsabe.+ Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+
10 Iye anatipulumutsadi ku chinthu choopsa, ndicho imfa, ndipo adzatipulumutsabe.+ Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+