Miyambo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+ Mlaliki 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+
4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+
18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+