Yakobo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tikamangirira zingwe+ pakamwa pa mahatchi* kuti atimvere,+ timatha kulamuliranso matupi awo onse.