Miyambo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Waulesi amati:+ “Panja pali mkango!+ Ndithu undipha pakati pa bwalo la mzinda!”