Yeremiya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abale ako komanso anthu a m’nyumba ya bambo ako akuchitira chinyengo,+ ndipo mofuula akukunenera zinthu zoipa ali kumbuyo kwako. Usawakhulupirire m’pang’ono pomwe, ngakhale kuti akukuuza mawu abwino.+
6 Abale ako komanso anthu a m’nyumba ya bambo ako akuchitira chinyengo,+ ndipo mofuula akukunenera zinthu zoipa ali kumbuyo kwako. Usawakhulupirire m’pang’ono pomwe, ngakhale kuti akukuuza mawu abwino.+