Luka 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anafika pomalakalaka chakudya cha nkhumbazo, ndipo palibe amene anali kum’patsa kanthu.+