Mlaliki 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zinthu zonse n’zotopetsa,+ ndipo palibe angazifotokoze. Diso silikhuta n’kuona,+ ndipo khutu silidzaza chifukwa cha kumva.+
8 Zinthu zonse n’zotopetsa,+ ndipo palibe angazifotokoze. Diso silikhuta n’kuona,+ ndipo khutu silidzaza chifukwa cha kumva.+