Luka 1:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.” Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.
79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.