Salimo 77:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke.
19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke.