Miyambo 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mkazi wachikoka amapeza ulemu.+ Koma anthu ochitira nkhanza anzawo amapeza chuma.