Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere. 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 koma aleke zoipa+ ndipo achite zabwino. Ayesetse kupeza mtendere ndi kuusunga.+