Miyambo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, usayende nawo limodzi panjira.+ Letsa phazi lako kuti lisayende panjira yawo.+