Mlaliki 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu a anthu anzeru ali ngati zisonga zobayira ng’ombe pozitsogolera,+ ndipo anthu amene amadzipereka kusonkhanitsa mawu anzeru, ali ngati misomali yokhomerera kwambiri.+ Mawuwo aperekedwa ndi m’busa mmodzi.+
11 Mawu a anthu anzeru ali ngati zisonga zobayira ng’ombe pozitsogolera,+ ndipo anthu amene amadzipereka kusonkhanitsa mawu anzeru, ali ngati misomali yokhomerera kwambiri.+ Mawuwo aperekedwa ndi m’busa mmodzi.+