Nehemiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+ Salimo 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zinthu zakuya.+ Miyambo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru.+ Kudziwa Woyera Koposa, ndiko kumvetsa zinthu.+
8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+
3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zinthu zakuya.+