Miyambo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, usayende nawo limodzi panjira.+ Letsa phazi lako kuti lisayende panjira yawo.+ Miyambo 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti munthu wochita zachiphamaso+ Yehova amanyansidwa naye,+ koma amakonda anthu owongoka mtima.+
32 Pakuti munthu wochita zachiphamaso+ Yehova amanyansidwa naye,+ koma amakonda anthu owongoka mtima.+