Yobu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma funsa nyama zoweta ndipo zikulangiza.+Komanso zouluka zam’mlengalenga, ndipo zikuuza.+