Miyambo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nyerere si zamphamvu,+ koma zimasonkhanitsa chakudya chawo m’chilimwe.+