Miyambo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kudzakupulumutsa kwa mkazi wachilendo, mkazi wochokera kwina+ wolankhula mwaukathyali,+ Miyambo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti hule lili ngati dzenje lakuya,+ ndipo mkazi wachilendo ali ngati chitsime chopapatiza.