Miyambo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zonse zimene umakonda sizingafanane nazo.