Salimo 85:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chilungamo chidzayenda pamaso pake,+Ndipo chidzapanga njira yotsatira mapazi a Mulungu.+ Miyambo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+
5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+