1 Mafumu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+ Miyambo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wonyoza amadana ndi munthu amene akum’dzudzula.+ Iye sadzapita kwa anthu anzeru.+
17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+