-
Mateyu 25:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Poyankha mbuye wakeyo anati, ‘Kapolo woipa ndi waulesi iwe! Ukuti unali kudziwa kuti ineyo ndimakolola kumene sindinafese ndi kututa tirigu kumene sindinapete?
-