Miyambo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zochita za wolungama zimabweretsa moyo.+ Zokolola za woipa zimabweretsa tchimo.+ Miyambo 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wosasunthika pachilungamo adzapeza moyo,+ koma munthu wofunafuna zoipa adzafa.+