Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+

  • Machitidwe 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+

  • Aheberi 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndipo tiyeni tiganizirane kuti tilimbikitsane+ pa chikondi ndi ntchito zabwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena