Miyambo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu owongoka mtima, iye amawasungira nzeru zopindulitsa.+ Kwa anthu oyenda ndi mtima wosagawanika, iye amakhala chishango+ Miyambo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+
7 Anthu owongoka mtima, iye amawasungira nzeru zopindulitsa.+ Kwa anthu oyenda ndi mtima wosagawanika, iye amakhala chishango+
9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+