Salimo 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zinthu zakuya.+ Miyambo 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+
3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zinthu zakuya.+
28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+