Deuteronomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo mawu awa amene ndikukulamula lero azikhala pamtima pako,+ Yobu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sindisiya malamulo otuluka pakamwa pake.+Ndasunga mosamala mawu a pakamwa pake+ kuposa zimene akufuna kuti ndichite.
12 Sindisiya malamulo otuluka pakamwa pake.+Ndasunga mosamala mawu a pakamwa pake+ kuposa zimene akufuna kuti ndichite.