Yobu 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinkawamwetulira, koma iwo sankakhulupirira,Ndipo kuwala kwa pankhope+ panga sankakuzimitsa. Machitidwe 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+
28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+