Miyambo 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wosaugwira mtima ali ngati mzinda umene mpanda wake wagumulidwa, n’kuusiya wopanda mpanda.+ Aroma 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musalole kuti choipa chikugonjetseni, koma pitirizani kugonjetsa choipa mwa kuchita chabwino.+
28 Munthu wosaugwira mtima ali ngati mzinda umene mpanda wake wagumulidwa, n’kuusiya wopanda mpanda.+