Miyambo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+
11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+