Miyambo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwala umalemera ndiponso mchenga umalemera ukaunyamula,+ koma kusautsa kwa munthu wopusa kumalemera kwambiri kuposa zonsezi.+
3 Mwala umalemera ndiponso mchenga umalemera ukaunyamula,+ koma kusautsa kwa munthu wopusa kumalemera kwambiri kuposa zonsezi.+