Miyambo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakamwa pa wolungama m’pamene pamachokera moyo,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+ Miyambo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Maganizo a mumtima mwa munthu ali ngati madzi akuya,+ koma munthu wozindikira ndi amene amawatunga.+
5 Maganizo a mumtima mwa munthu ali ngati madzi akuya,+ koma munthu wozindikira ndi amene amawatunga.+