2 Samueli 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Abisalomu anapitiriza kukhala m’Yerusalemu zaka ziwiri zathunthu, ndipo sanaonane ndi mfumu.+ Machitidwe 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo panabuka mkangano woopsa mpaka anapatukana. Baranaba+ anatenga Maliko ndipo anayenda ulendo wa pamadzi kulowera ku Kupuro.+
39 Pamenepo panabuka mkangano woopsa mpaka anapatukana. Baranaba+ anatenga Maliko ndipo anayenda ulendo wa pamadzi kulowera ku Kupuro.+