Yoweli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Anthu inu, lengezani pakati pa mitundu ina kuti,+ ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu!+ Amuna onse ankhondo abwere!+
9 “Anthu inu, lengezani pakati pa mitundu ina kuti,+ ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu!+ Amuna onse ankhondo abwere!+