Mlaliki 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimene zinalipo n’zimene zidzakhaleponso+ ndipo zimene zinachitidwa n’zimene zidzachitidwenso. Choncho palibe chatsopano padziko lapansi pano.+
9 Zimene zinalipo n’zimene zidzakhaleponso+ ndipo zimene zinachitidwa n’zimene zidzachitidwenso. Choncho palibe chatsopano padziko lapansi pano.+