2 Samueli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+
10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+