Mlaliki 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mawu a wosonkhanitsa anthu,+ mwana wa Davide, mfumu ya ku Yerusalemu.+ Mlaliki 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine wosonkhanitsa, ndinali mfumu ya Isiraeli ku Yerusalemu.+