Salimo 119:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo sindikanachita manyazi,+Pamene ndikulabadira malamulo anu onse.+ Aroma 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda. Aroma 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero pali chifukwa chabwino chakuti anthu inu mukhalire ogonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyo umenewo, komanso chifukwa cha chikumbumtima chanu.+ 1 Petulo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, ndani angakuchitireni zoipa mukakhala odzipereka pochita zabwino?+
3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda.
5 Chotero pali chifukwa chabwino chakuti anthu inu mukhalire ogonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyo umenewo, komanso chifukwa cha chikumbumtima chanu.+