Luka 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’masiku amenewo anthu anali kudya, kumwa, amuna anali kukwatira, akazi anali kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m’chingalawa, ndipo chigumula chinafika ndi kuwononga anthu onsewo.+ Luka 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma tsiku limene Loti anatuluka mu Sodomu, kumwamba kunagwa moto ndi sulufule ngati mvula n’kuwononga anthu onse.+
27 M’masiku amenewo anthu anali kudya, kumwa, amuna anali kukwatira, akazi anali kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m’chingalawa, ndipo chigumula chinafika ndi kuwononga anthu onsewo.+
29 Koma tsiku limene Loti anatuluka mu Sodomu, kumwamba kunagwa moto ndi sulufule ngati mvula n’kuwononga anthu onse.+