Mateyu 24:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pa chifukwa chimenechi, nanunso khalani okonzeka,+ chifukwa pa ola limene simukuliganizira, Mwana wa munthu adzabwera.
44 Pa chifukwa chimenechi, nanunso khalani okonzeka,+ chifukwa pa ola limene simukuliganizira, Mwana wa munthu adzabwera.