Yobu 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akaika mtima wake pa munthu aliyense,Akatenga mzimu* ndi mpweya wa munthuyo,+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
14 Akaika mtima wake pa munthu aliyense,Akatenga mzimu* ndi mpweya wa munthuyo,+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+