Mlaliki 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndifunefune ndi kufufuza nzeru+ mogwirizana ndi zonse zimene zachitidwa padziko lapansi, kutanthauza ntchito yosautsa mtima imene Mulungu wapatsa ana a anthu kuti azigwira.+
13 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndifunefune ndi kufufuza nzeru+ mogwirizana ndi zonse zimene zachitidwa padziko lapansi, kutanthauza ntchito yosautsa mtima imene Mulungu wapatsa ana a anthu kuti azigwira.+