Miyambo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usamadzione kuti ndiwe wanzeru.+ Uziopa Yehova ndi kupatuka pa choipa.+ Miyambo 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzimuyankha wopusa mogwirizana ndi uchitsiru wake, kuti asadzione ngati wanzeru m’maso mwake.+