Mlaliki 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri: Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Kodi pali phindu lanji kwa munthu amene amachita khama kugwirira ntchito mphepo?+
16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri: Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Kodi pali phindu lanji kwa munthu amene amachita khama kugwirira ntchito mphepo?+