Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+ Ezekieli 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+
21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+