Nyimbo ya Solomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Undipsompsone ndi milomo yako,+ chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo kukoma kwake.+ Nyimbo ya Solomo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nditenge,+ tiye tithawe! Chifukwatu mfumu yandipititsa m’zipinda zake zamkati.+ Tiye tikondwere ndi kusangalalira limodzi. Tiye tinene za chikondi chimene umandisonyeza osati za vinyo.+ M’pake kuti atsikana amakukonda.+
2 “Undipsompsone ndi milomo yako,+ chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo kukoma kwake.+
4 Nditenge,+ tiye tithawe! Chifukwatu mfumu yandipititsa m’zipinda zake zamkati.+ Tiye tikondwere ndi kusangalalira limodzi. Tiye tinene za chikondi chimene umandisonyeza osati za vinyo.+ M’pake kuti atsikana amakukonda.+