1 Mafumu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka n’kumapita ndipo anafika ku Tiriza.+ Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira.
17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka n’kumapita ndipo anafika ku Tiriza.+ Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira.